Yeremiya 51:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Munthu wodziwa kuponya mivi musamulole kukunga uta wake. Musalole kuti aliyense aimirire atavala chovala chamamba achitsulo. Anyamata ake musawamvere chisoni.+ Wonongani gulu lake lonse la asilikali.
3 Munthu wodziwa kuponya mivi musamulole kukunga uta wake. Musalole kuti aliyense aimirire atavala chovala chamamba achitsulo. Anyamata ake musawamvere chisoni.+ Wonongani gulu lake lonse la asilikali.