Yeremiya 51:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa Mulungu, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, sanasiye Isiraeli ndi Yuda kuti akhale akazi amasiye.+ Koma dziko la Akasidi lili ndi mlandu waukulu pamaso pa Woyera wa Isiraeli.
5 Chifukwa Mulungu, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, sanasiye Isiraeli ndi Yuda kuti akhale akazi amasiye.+ Koma dziko la Akasidi lili ndi mlandu waukulu pamaso pa Woyera wa Isiraeli.