Yeremiya 51:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Nolani mivi yanu.*+ Tengani zishango zozungulira. Yehova walimbikitsa* mafumu a Amedi kuti akamenye nkhondo,+Chifukwa akufuna kuwononga Babulo. Yehova akubwezera Babulo, akumubwezera chifukwa cha kachisi wake. Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 51:11 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,6/2017, tsa. 3
11 “Nolani mivi yanu.*+ Tengani zishango zozungulira. Yehova walimbikitsa* mafumu a Amedi kuti akamenye nkhondo,+Chifukwa akufuna kuwononga Babulo. Yehova akubwezera Babulo, akumubwezera chifukwa cha kachisi wake.