Yeremiya 51:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba walumbira mʼdzina lake kuti,‘Mʼdziko lako ndidzadzazamo amuna ochuluka ngati dzombe,Ndipo amunawo adzafuula mosangalala chifukwa chakuti akugonjetsa.’+
14 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba walumbira mʼdzina lake kuti,‘Mʼdziko lako ndidzadzazamo amuna ochuluka ngati dzombe,Ndipo amunawo adzafuula mosangalala chifukwa chakuti akugonjetsa.’+