Yeremiya 51:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mawu ake akamveka,Madzi akumwamba amachita mkokomo,Ndipo amachititsa mitambo* kukwera kuchokera kumalekezero a dziko lapansi. Iye amachititsa kuti kukamagwa mvula mphezi zizingʼanimaNdipo amatulutsa mphepo mʼnyumba zake zosungira.+
16 Mawu ake akamveka,Madzi akumwamba amachita mkokomo,Ndipo amachititsa mitambo* kukwera kuchokera kumalekezero a dziko lapansi. Iye amachititsa kuti kukamagwa mvula mphezi zizingʼanimaNdipo amatulutsa mphepo mʼnyumba zake zosungira.+