Yeremiya 51:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo ndi achabechabe,+ oyenera kunyozedwa. Tsiku loti aweruzidwe likadzafika adzawonongedwa.