Yeremiya 51:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma Mulungu, amene ndi cholowa cha Yakobo, sali ngati mafano amenewa,Chifukwa iye ndi amene anapanga chilichonse,Ngakhalenso ndodo ya cholowa chake.+ Dzina lake ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.”+
19 Koma Mulungu, amene ndi cholowa cha Yakobo, sali ngati mafano amenewa,Chifukwa iye ndi amene anapanga chilichonse,Ngakhalenso ndodo ya cholowa chake.+ Dzina lake ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.”+