-
Yeremiya 51:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 “Iwe ndiwe chibonga changa, chida changa chomenyera nkhondo,
Ndipo ndidzakugwiritsa ntchito pophwanya mitundu ya anthu.
Ndidzakugwiritsa ntchito powononga maufumu.
-