-
Yeremiya 51:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Ndidzakugwiritsa ntchito pophwanya hatchi ndi wokwerapo wake.
Ndidzakugwiritsa ntchito pophwanya magaleta ankhondo ndi okweramo ake.
-