Yeremiya 51:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Sankhani* mitundu ya anthu kuti ichite naye nkhondo.Sankhani mafumu a ku Mediya,+ abwanamkubwa ake ndi achiwiri kwa olamulira awo onseKomanso mayiko onse amene iwo amawalamulira.
28 Sankhani* mitundu ya anthu kuti ichite naye nkhondo.Sankhani mafumu a ku Mediya,+ abwanamkubwa ake ndi achiwiri kwa olamulira awo onseKomanso mayiko onse amene iwo amawalamulira.