Yeremiya 51:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Dziko lidzagwedezeka ndi kunjenjemera,Chifukwa Yehova adzachitira Babulo zimene akuganizaKuti dziko la Babulo likhale chinthu chochititsa mantha, lopanda munthu wokhalamo.+
29 Dziko lidzagwedezeka ndi kunjenjemera,Chifukwa Yehova adzachitira Babulo zimene akuganizaKuti dziko la Babulo likhale chinthu chochititsa mantha, lopanda munthu wokhalamo.+