Yeremiya 51:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Asilikali a ku Babulo asiya kumenya nkhondo. Iwo akhala pansi mʼmalo awo otetezeka. Mphamvu zawo zatha.+ Akhala ngati akazi.+ Nyumba za mʼBabulo zawotchedwa. Mipiringidzo yake yathyoledwa.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 51:30 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,6/2017, tsa. 3 Yeremiya, ptsa. 161-162 Mawu a Mulungu, ptsa. 123, 124-125 Nsanja ya Olonda,3/1/1988, tsa. 31
30 Asilikali a ku Babulo asiya kumenya nkhondo. Iwo akhala pansi mʼmalo awo otetezeka. Mphamvu zawo zatha.+ Akhala ngati akazi.+ Nyumba za mʼBabulo zawotchedwa. Mipiringidzo yake yathyoledwa.+
51:30 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,6/2017, tsa. 3 Yeremiya, ptsa. 161-162 Mawu a Mulungu, ptsa. 123, 124-125 Nsanja ya Olonda,3/1/1988, tsa. 31