Yeremiya 51:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Munthu amene watumidwa kukanena uthenga wakumana ndi mnzake,Ndipo mthenga wina wakumana ndi mnzake.Onsewa akukanena kwa mfumu ya Babulo kuti mzinda wake walandidwa kumbali zonse.+
31 Munthu amene watumidwa kukanena uthenga wakumana ndi mnzake,Ndipo mthenga wina wakumana ndi mnzake.Onsewa akukanena kwa mfumu ya Babulo kuti mzinda wake walandidwa kumbali zonse.+