Yeremiya 51:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Mwana wamkazi wa Babulo* ali ngati malo opunthira mbewu. Ino ndi nthawi yomupondaponda. Posachedwapa nthawi yokolola imufikira.”
33 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Mwana wamkazi wa Babulo* ali ngati malo opunthira mbewu. Ino ndi nthawi yomupondaponda. Posachedwapa nthawi yokolola imufikira.”