Yeremiya 51:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Anthu amene akukhala mu Ziyoni akunena kuti, ‘Chiwawa chimene anachitira ine ndi thupi langa chigwerenso Babulo.’+ Ndipo Yerusalemu akunena kuti, ‘Magazi anga akhale pa anthu amene akukhala mʼdziko la Kasidi.’”
35 Anthu amene akukhala mu Ziyoni akunena kuti, ‘Chiwawa chimene anachitira ine ndi thupi langa chigwerenso Babulo.’+ Ndipo Yerusalemu akunena kuti, ‘Magazi anga akhale pa anthu amene akukhala mʼdziko la Kasidi.’”