Yeremiya 51:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 “Akadzakhala ndi chilakolako champhamvu chofuna kudya, ndidzawakonzera phwando ndipo ndidzawaledzeretsaNʼcholinga choti asangalale.+Kenako adzagona tulo tosathaNdipo sadzadzukanso,”+ akutero Yehova.
39 “Akadzakhala ndi chilakolako champhamvu chofuna kudya, ndidzawakonzera phwando ndipo ndidzawaledzeretsaNʼcholinga choti asangalale.+Kenako adzagona tulo tosathaNdipo sadzadzukanso,”+ akutero Yehova.