Yeremiya 51:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Mizinda yake yakhala chinthu chochititsa mantha, dziko lopanda madzi komanso chipululu. Mizindayo yakhala dziko limene simudzakhalanso munthu aliyense ndipo palibe munthu amene adzadutsemo.+
43 Mizinda yake yakhala chinthu chochititsa mantha, dziko lopanda madzi komanso chipululu. Mizindayo yakhala dziko limene simudzakhalanso munthu aliyense ndipo palibe munthu amene adzadutsemo.+