Yeremiya 51:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Tulukani mʼBabulo anthu anga.+ Thawani mkwiyo wa Yehova+ woyaka moto kuti mupulumutse moyo wanu.+