Yeremiya 51:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Choncho masiku adzafikaPamene ndidzawononge zifaniziro zogoba za ku Babulo. Dziko lake lonse lidzachititsidwa manyazi,Ndipo mitembo ya anthu ake onse amene adzaphedwe idzakhala paliponse mumzindawo.+
47 Choncho masiku adzafikaPamene ndidzawononge zifaniziro zogoba za ku Babulo. Dziko lake lonse lidzachititsidwa manyazi,Ndipo mitembo ya anthu ake onse amene adzaphedwe idzakhala paliponse mumzindawo.+