Yeremiya 51:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Kumwamba ndi dziko lapansi komanso chilichonse cha mmenemoZidzafuula mosangalala poona kuti Babulo wagwa,+Chifukwa owononga adzabwera kwa iye kuchokera kumpoto,”+ akutero Yehova.
48 Kumwamba ndi dziko lapansi komanso chilichonse cha mmenemoZidzafuula mosangalala poona kuti Babulo wagwa,+Chifukwa owononga adzabwera kwa iye kuchokera kumpoto,”+ akutero Yehova.