Yeremiya 51:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 “Choncho masiku adzafika,” akutero Yehova,“Pamene ndidzawononge zifaniziro zake zogoba,Ndipo mʼdziko lake lonse anthu ovulazidwa adzakhala akubuula.”+
52 “Choncho masiku adzafika,” akutero Yehova,“Pamene ndidzawononge zifaniziro zake zogoba,Ndipo mʼdziko lake lonse anthu ovulazidwa adzakhala akubuula.”+