Yeremiya 51:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 “Ngakhale Babulo atakwera kukafika kumwamba,+Ngakhale atalimbitsa kwambiri mpanda wake wautaliwo,Anthu amene adzamuwononge adzabwera kuchokera kwa ine,”+ akutero Yehova.
53 “Ngakhale Babulo atakwera kukafika kumwamba,+Ngakhale atalimbitsa kwambiri mpanda wake wautaliwo,Anthu amene adzamuwononge adzabwera kuchokera kwa ine,”+ akutero Yehova.