-
Yeremiya 51:55Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
55 Chifukwa Yehova akuwononga Babulo,
Adzachititsa kuti mawu ake aakuluwo asamvekenso,
Ndipo phokoso la adani ake lidzakhala ngati la mafunde amphamvu.
Phokoso la mawu awo lidzamveka.
-