Yeremiya 51:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Ndidzaledzeretsa akalonga ake, anthu ake anzeru,+Abwanamkubwa ake, achiwiri kwa olamulira ake ndi asilikali ake,Ndipo adzagona tulo tosatha,Moti sadzadzukanso,”+ ikutero Mfumu, imene dzina lake ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
57 Ndidzaledzeretsa akalonga ake, anthu ake anzeru,+Abwanamkubwa ake, achiwiri kwa olamulira ake ndi asilikali ake,Ndipo adzagona tulo tosatha,Moti sadzadzukanso,”+ ikutero Mfumu, imene dzina lake ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.