Yeremiya 51:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Mneneri Yeremiya anapereka malangizo kwa Seraya mwana wa Neriya+ mwana wa Maseya. Anapereka malangizowo pamene Seraya anapita ndi Zedekiya mfumu ya Yuda ku Babulo mʼchaka cha 4 cha ufumu wake. Seraya anali woyangʼanira zinthu za mfumu.
59 Mneneri Yeremiya anapereka malangizo kwa Seraya mwana wa Neriya+ mwana wa Maseya. Anapereka malangizowo pamene Seraya anapita ndi Zedekiya mfumu ya Yuda ku Babulo mʼchaka cha 4 cha ufumu wake. Seraya anali woyangʼanira zinthu za mfumu.