-
Yeremiya 51:60Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
60 Yeremiya analemba mʼbuku limodzi masoka onse amene adzagwere Babulo. Iye analemba mawu onsewa okhudza zimene zidzachitikire Babulo.
-