Yeremiya 51:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Kenako ukanene kuti, ‘Inu Yehova! Inu mwanena kuti malo ano adzawonongedwa ndipo simudzapezeka aliyense wokhalamo, munthu kapena nyama, komanso kuti mzindawu udzakhala bwinja mpaka kalekale.’+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 51:62 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,6/2017, tsa. 3
62 Kenako ukanene kuti, ‘Inu Yehova! Inu mwanena kuti malo ano adzawonongedwa ndipo simudzapezeka aliyense wokhalamo, munthu kapena nyama, komanso kuti mzindawu udzakhala bwinja mpaka kalekale.’+