Yeremiya 51:64 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 64 Ndiyeno ukanene kuti, ‘Umu ndi mmene Babulo adzamirire ndipo sadzatulukanso+ chifukwa cha tsoka limene ndikumugwetsera. Ndipo anthu amene akukhala mumzindawo adzatopa.’”+ Mawu a Yeremiya athera pamenepa. Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 51:64 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 269
64 Ndiyeno ukanene kuti, ‘Umu ndi mmene Babulo adzamirire ndipo sadzatulukanso+ chifukwa cha tsoka limene ndikumugwetsera. Ndipo anthu amene akukhala mumzindawo adzatopa.’”+ Mawu a Yeremiya athera pamenepa.