Yeremiya 52:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma asilikali a Akasidi anayamba kuthamangitsa Zedekiya+ ndipo anamupeza mʼchipululu cha Yeriko. Zitatero asilikali onse a mfumuyo anabalalika nʼkuisiya yokha.
8 Koma asilikali a Akasidi anayamba kuthamangitsa Zedekiya+ ndipo anamupeza mʼchipululu cha Yeriko. Zitatero asilikali onse a mfumuyo anabalalika nʼkuisiya yokha.