-
Yeremiya 52:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Ndipo mfumu ya Babulo inapha ana aamuna a Zedekiya, iye akuona. Inaphanso akalonga onse a ku Yuda ku Ribila komweko.
-