Yeremiya 52:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako mfumu ya Babulo inachititsa khungu Zedekiya,+ inamumanga ndi maunyolo akopa* nʼkupita naye ku Babulo ndipo inamuika mʼndende mpaka tsiku la imfa yake. Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 52:11 Yeremiya, ptsa. 158-159
11 Kenako mfumu ya Babulo inachititsa khungu Zedekiya,+ inamumanga ndi maunyolo akopa* nʼkupita naye ku Babulo ndipo inamuika mʼndende mpaka tsiku la imfa yake.