Yeremiya 52:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mʼmwezi wa 5, pa tsiku la 10 la mweziwo, chomwe chinali chaka cha 19 cha Mfumu Nebukadinezara* ya ku Babulo, Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu, amene anali mtumiki wa mfumu ya Babulo, anabwera ku Yerusalemu.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 52:12 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 11
12 Mʼmwezi wa 5, pa tsiku la 10 la mweziwo, chomwe chinali chaka cha 19 cha Mfumu Nebukadinezara* ya ku Babulo, Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu, amene anali mtumiki wa mfumu ya Babulo, anabwera ku Yerusalemu.+