Yeremiya 52:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako asilikali onse a Akasidi, omwe anali ndi mkulu wa asilikali olondera mfumu uja, anagwetsa mpanda wonse wa Yerusalemu.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 52:14 Yeremiya, tsa. 159
14 Kenako asilikali onse a Akasidi, omwe anali ndi mkulu wa asilikali olondera mfumu uja, anagwetsa mpanda wonse wa Yerusalemu.+