Yeremiya 52:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ena mwa anthu osauka kwambiri amʼdzikolo, Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anawasiya kuti akhale olima minda ya mpesa ndi anthu ogwira ntchito mokakamizidwa.+
16 Ena mwa anthu osauka kwambiri amʼdzikolo, Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anawasiya kuti akhale olima minda ya mpesa ndi anthu ogwira ntchito mokakamizidwa.+