Yeremiya 52:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Akasidi anaphwanyaphwanya zipilala zakopa+ zapanyumba ya Yehova, zotengera zokhala ndi mawilo+ ndiponso thanki yakopa yosungira madzi+ zimene zinali mʼnyumba ya Yehova nʼkutenga kopa yense kupita naye ku Babulo.+
17 Akasidi anaphwanyaphwanya zipilala zakopa+ zapanyumba ya Yehova, zotengera zokhala ndi mawilo+ ndiponso thanki yakopa yosungira madzi+ zimene zinali mʼnyumba ya Yehova nʼkutenga kopa yense kupita naye ku Babulo.+