Yeremiya 52:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Akasidiwo anatenganso ndowa, mafosholo, zozimitsira nyale, mbale zolowa,+ makapu+ ndi ziwiya zonse zakopa zimene ansembe ankagwiritsa ntchito potumikira mʼkachisi.
18 Akasidiwo anatenganso ndowa, mafosholo, zozimitsira nyale, mbale zolowa,+ makapu+ ndi ziwiya zonse zakopa zimene ansembe ankagwiritsa ntchito potumikira mʼkachisi.