Yeremiya 52:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anatenga mabeseni,+ zopalira moto, mbale zolowa, ndowa zochotsera phulusa, zoikapo nyale,+ makapu ndi mbale zinanso zolowa zomwe zinali zagolide komanso zasiliva weniweni.+
19 Mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anatenga mabeseni,+ zopalira moto, mbale zolowa, ndowa zochotsera phulusa, zoikapo nyale,+ makapu ndi mbale zinanso zolowa zomwe zinali zagolide komanso zasiliva weniweni.+