-
Yeremiya 52:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Koma zinali zosatheka kuyeza kulemera kwa kopa wa zipilala ziwiri zija, thanki yosungira madzi, ngʼombe zakopa 12+ zimene zinali pansi pa thanki yosungira madzi ndiponso zotengera zokhala ndi mawilo zimene Mfumu Solomo anapanga kuti zizigwira ntchito panyumba ya Yehova chifukwa anali wochuluka kwambiri.
-