Yeremiya 52:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ponena za zipilalazo, chipilala chilichonse chinali chachitali mamita 8* ndipo chinkatha kuzunguliridwa ndi chingwe chachitali mamita 5.*+ Chipilala chilichonse chinali ndi mphako mkati ndipo kuchindikala kwake kunali masentimita 7.*
21 Ponena za zipilalazo, chipilala chilichonse chinali chachitali mamita 8* ndipo chinkatha kuzunguliridwa ndi chingwe chachitali mamita 5.*+ Chipilala chilichonse chinali ndi mphako mkati ndipo kuchindikala kwake kunali masentimita 7.*