Yeremiya 52:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mutu wa chipilala chilichonse unali wakopa. Mutuwo unali wautali mamita awiri*+ ndipo maukonde ndi makangaza* amene anazungulira mutuwo, onse anali akopa. Chipilala chachiwiri chinali chofanana ndi choyambacho, chimodzimodzinso makangaza ake.
22 Mutu wa chipilala chilichonse unali wakopa. Mutuwo unali wautali mamita awiri*+ ndipo maukonde ndi makangaza* amene anazungulira mutuwo, onse anali akopa. Chipilala chachiwiri chinali chofanana ndi choyambacho, chimodzimodzinso makangaza ake.