Yeremiya 52:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mʼchaka cha 23 cha ulamuliro wa Nebukadinezara,* Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu anatenga Ayuda 745 kupita nawo ku ukapolo.+ Anthu onse amene anatengedwa kupita ku ukapolo anali 4,600.
30 Mʼchaka cha 23 cha ulamuliro wa Nebukadinezara,* Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu anatenga Ayuda 745 kupita nawo ku ukapolo.+ Anthu onse amene anatengedwa kupita ku ukapolo anali 4,600.