Yeremiya 52:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako mʼchaka cha 37 cha ukapolo wa Yehoyakini+ mfumu ya Yuda, Evili-merodaki anakhala mfumu ya Babulo. Ndiyeno mʼchaka chomwecho mʼmwezi wa 12, pa tsiku la 25 la mweziwo, iye anamasula* Yehoyakini mfumu ya Yuda nʼkumutulutsa mʼndende.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 52:31 Yeremiya, tsa. 31
31 Kenako mʼchaka cha 37 cha ukapolo wa Yehoyakini+ mfumu ya Yuda, Evili-merodaki anakhala mfumu ya Babulo. Ndiyeno mʼchaka chomwecho mʼmwezi wa 12, pa tsiku la 25 la mweziwo, iye anamasula* Yehoyakini mfumu ya Yuda nʼkumutulutsa mʼndende.+