Maliro 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye akulira kwambiri usiku+ ndipo misozi ikutsika mʼmasaya ake. Pa anthu onse amene ankamukonda, palibe aliyense amene akumutonthoza.+ Anzake onse amuchitira zachinyengo+ ndipo asanduka adani ake. Maliro Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:2 Nsanja ya Olonda,9/1/1988, tsa. 26
2 Iye akulira kwambiri usiku+ ndipo misozi ikutsika mʼmasaya ake. Pa anthu onse amene ankamukonda, palibe aliyense amene akumutonthoza.+ Anzake onse amuchitira zachinyengo+ ndipo asanduka adani ake.