Maliro 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yuda watengedwa kupita kudziko lina+ ndipo akuvutika komanso akugwira ntchito yaukapolo.+ Iye akuyenera kukhala pakati pa mitundu ina ya anthu+ ndipo sanapeze malo oti azikhala mwamtendere. Onse amene amamufunafuna amupeza ali pamavuto.
3 Yuda watengedwa kupita kudziko lina+ ndipo akuvutika komanso akugwira ntchito yaukapolo.+ Iye akuyenera kukhala pakati pa mitundu ina ya anthu+ ndipo sanapeze malo oti azikhala mwamtendere. Onse amene amamufunafuna amupeza ali pamavuto.