Maliro 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano adani ake akumulamulira. Iwo sakuda nkhawa.+ Yehova wamuchititsa kuti akhale ndi chisoni chifukwa cha kuchuluka kwa machimo ake.+ Ana ake agwidwa ndi adani ndipo atengedwa kupita ku ukapolo.+
5 Tsopano adani ake akumulamulira. Iwo sakuda nkhawa.+ Yehova wamuchititsa kuti akhale ndi chisoni chifukwa cha kuchuluka kwa machimo ake.+ Ana ake agwidwa ndi adani ndipo atengedwa kupita ku ukapolo.+