7 Pa nthawi imene ankazunzika komanso pamene ankasowa pokhala, Yerusalemu anakumbukira
Zinthu zake zonse zamtengo wapatali zimene anali nazo kalekale.+
Anthu ake atagwidwa ndi adani moti panalibe munthu woti amuthandize,+
Adaniwo anamuona ndipo anamuseka chifukwa chakuti wagwa.+