Maliro 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zovala zake zadetsedwa. Iye sanaganizire za tsogolo lake.+ Wagwa modabwitsa ndipo palibe aliyense woti amutonthoze. Inu Yehova, onani kuvutika kwanga, chifukwa mdani wanga akudzitukumula.+
9 Zovala zake zadetsedwa. Iye sanaganizire za tsogolo lake.+ Wagwa modabwitsa ndipo palibe aliyense woti amutonthoze. Inu Yehova, onani kuvutika kwanga, chifukwa mdani wanga akudzitukumula.+