Maliro 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mdani wamulanda zinthu zake zonse zamtengo wapatali.+ Yerusalemu waona anthu a mitundu ina akulowa mʼmalo ake opatulika,+Mitundu imene munalamula kuti isamalowe mumpingo wanu.
10 Mdani wamulanda zinthu zake zonse zamtengo wapatali.+ Yerusalemu waona anthu a mitundu ina akulowa mʼmalo ake opatulika,+Mitundu imene munalamula kuti isamalowe mumpingo wanu.