Maliro 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu ake onse akuusa moyo. Iwo akufunafuna chakudya.+ Asinthanitsa zinthu zawo zamtengo wapatali ndi chakudya kuti akhale ndi moyo. Inu Yehova ndiyangʼaneni. Onani kuti ndakhala ngati mkazi* wachabechabe.
11 Anthu ake onse akuusa moyo. Iwo akufunafuna chakudya.+ Asinthanitsa zinthu zawo zamtengo wapatali ndi chakudya kuti akhale ndi moyo. Inu Yehova ndiyangʼaneni. Onani kuti ndakhala ngati mkazi* wachabechabe.