12 Inu nonse amene mukudutsa munsewu, kodi mukuona ngati imeneyi ndi nkhani yaingʼono?
Ndiyangʼaneni kuti muone.
Kodi palinso ululu wina woposa ululu umene ndikumva chifukwa cholangidwa,
Ululu umene Yehova wachititsa kuti ndiumve pa tsiku la mkwiyo wake woyaka moto?+